Yoswa 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ankalamuliranso ku Araba mpaka kunyanja ya Kinereti*+ chakumʼmawa kwa nyanjayi, mpaka kukafika kunyanja ya Araba, yomwe ndi Nyanja Yamchere.* Komanso ankalamulira kumʼmawa, cha ku Beti-yesimoti ndiponso chakumʼmwera, kumunsi kwa Pisiga.+
3 Ankalamuliranso ku Araba mpaka kunyanja ya Kinereti*+ chakumʼmawa kwa nyanjayi, mpaka kukafika kunyanja ya Araba, yomwe ndi Nyanja Yamchere.* Komanso ankalamulira kumʼmawa, cha ku Beti-yesimoti ndiponso chakumʼmwera, kumunsi kwa Pisiga.+