Yoswa 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ankalamulira kuphiri la Herimoni, ku Saleka ndi ku Basana+ konse, mpaka kukafika kumalire a Agesuri ndi Amaakati.+ Ankalamuliranso hafu ya Giliyadi mpaka kumalire ndi dera limene Sihoni, mfumu ya Hesiboni, ankalamulira.+
5 Ankalamulira kuphiri la Herimoni, ku Saleka ndi ku Basana+ konse, mpaka kukafika kumalire a Agesuri ndi Amaakati.+ Ankalamuliranso hafu ya Giliyadi mpaka kumalire ndi dera limene Sihoni, mfumu ya Hesiboni, ankalamulira.+