Yoswa 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose mtumiki wa Yehova ndi Aisiraeli anagonjetsa mafumuwa.+ Kenako Mose mtumiki wa Yehova anapereka maderawa kwa fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase kuti akhale awo.+
6 Mose mtumiki wa Yehova ndi Aisiraeli anagonjetsa mafumuwa.+ Kenako Mose mtumiki wa Yehova anapereka maderawa kwa fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase kuti akhale awo.+