Yoswa 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano Yoswa anali atakalamba, ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Choncho Yehova anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba ndipo uli ndi zaka zambiri, koma madera oti alandidwe adakali ambiri. Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:1 Nsanja ya Olonda,12/1/2004, tsa. 11
13 Tsopano Yoswa anali atakalamba, ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Choncho Yehova anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba ndipo uli ndi zaka zambiri, koma madera oti alandidwe adakali ambiri.