Yoswa 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Madera amene atsala ndi awa:+ Madera onse a Afilisiti ndi madera onse a Agesuri.+