3 (Dera loyambira kukamtsinje kotuluka mu Nailo kumʼmawa kwa Iguputo, kukafika kumpoto kumalire ndi Ekironi, lomwe linkaonedwa kuti ndi la Akanani.)+ Komanso madera a olamulira 5 a Afilisiti+ omwe ndi Gaza, Asidodi,+ Asikeloni,+ Gati+ ndi Ekironi,+ ndiponso dera la Aavimu.+