Yoswa 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Dera lawo linali mzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi komanso hafu ya dziko la Aamoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli kufupi ndi Raba.+
25 Dera lawo linali mzinda wa Yazeri,+ mizinda yonse ya ku Giliyadi komanso hafu ya dziko la Aamoni,+ mpaka kukafika ku Aroweli kufupi ndi Raba.+