Yoswa 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aisiraeli anatenga cholowa chawo mʼdziko la Kanani. Wansembe Eliezara, Yoswa mwana wa Nuni ndi atsogoleri a mafuko a makolo a Aisiraeli ndi amene anawagawira cholowachi.+
14 Aisiraeli anatenga cholowa chawo mʼdziko la Kanani. Wansembe Eliezara, Yoswa mwana wa Nuni ndi atsogoleri a mafuko a makolo a Aisiraeli ndi amene anawagawira cholowachi.+