Yoswa 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana a Yosefe anali mafuko awiri,+ la Manase ndi la Efuraimu.+ Alevi sanapatsidwe cholowa cha malo koma anangowapatsa mizinda+ yoti azikhalamo komanso malo odyetserako ziweto ndi osungirako katundu wawo.+
4 Ana a Yosefe anali mafuko awiri,+ la Manase ndi la Efuraimu.+ Alevi sanapatsidwe cholowa cha malo koma anangowapatsa mizinda+ yoti azikhalamo komanso malo odyetserako ziweto ndi osungirako katundu wawo.+