Yoswa 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano amuna a ku Yuda anapita kwa Yoswa ku Giligala.+ Ndipo Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi, anauza Yoswa kuti: “Inu mukudziwa bwino zimene Yehova anauza+ Mose, munthu wa Mulungu woona,+ ku Kadesi-barinea zokhudza ine ndi inu.+
6 Tsopano amuna a ku Yuda anapita kwa Yoswa ku Giligala.+ Ndipo Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi, anauza Yoswa kuti: “Inu mukudziwa bwino zimene Yehova anauza+ Mose, munthu wa Mulungu woona,+ ku Kadesi-barinea zokhudza ine ndi inu.+