Yoswa 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale kuti abale anga amene ndinali nawo, anapangitsa anthu kuchita mantha kwambiri,* ine ndinatsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:8 Nsanja ya Olonda,5/15/1993, ptsa. 26-29
8 Ngakhale kuti abale anga amene ndinali nawo, anapangitsa anthu kuchita mantha kwambiri,* ine ndinatsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.+