-
Yoswa 14:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Choncho ndipatseni dera lamapiri ili limene Yehova anandilonjeza tsiku limene lija. Ngakhale kuti pa tsikulo, munamva kuti kumeneko kuli Aanaki+ komanso mizinda ikuluikulu yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ sindikukayikira kuti Yehova adzakhala nane,+ ndipo ndikawathamangitsa ndithu ngati mmene Yehova analonjezera.”+
-