Yoswa 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nʼchifukwa chake mzinda wa Heburoni unakhala cholowa cha Kalebe mwana wa Yefune Mkenizi, mpaka lero, chifukwa iye anatsatira Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mtima wake wonse.+
14 Nʼchifukwa chake mzinda wa Heburoni unakhala cholowa cha Kalebe mwana wa Yefune Mkenizi, mpaka lero, chifukwa iye anatsatira Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mtima wake wonse.+