Yoswa 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Malirewo analowera kumʼmwera kuchitunda cha Akirabimu+ nʼkukafika ku Zini. Kenako anakwera kuchokera kumʼmwera kupita ku Kadesi-barinea,+ nʼkukafika ku Hezironi mpaka ku Adara, nʼkuzungulira kukafika cha ku Karika.
3 Malirewo analowera kumʼmwera kuchitunda cha Akirabimu+ nʼkukafika ku Zini. Kenako anakwera kuchokera kumʼmwera kupita ku Kadesi-barinea,+ nʼkukafika ku Hezironi mpaka ku Adara, nʼkuzungulira kukafika cha ku Karika.