Yoswa 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anakafika ku Debiri kuchigwa cha Akori+ nʼkukhotera kumpoto cha ku Giligala,+ patsogolo pa chitunda cha Adumi, kumʼmwera kwa chigwa cha mtsinje. Malirewo anapitirira nʼkukafika kumadzi a Eni-semesi,+ nʼkukathera ku Eni-rogeli.+
7 Anakafika ku Debiri kuchigwa cha Akori+ nʼkukhotera kumpoto cha ku Giligala,+ patsogolo pa chitunda cha Adumi, kumʼmwera kwa chigwa cha mtsinje. Malirewo anapitirira nʼkukafika kumadzi a Eni-semesi,+ nʼkukathera ku Eni-rogeli.+