Yoswa 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Malirewo anakafika kumalo otsetsereka otchedwa Ekironi+ kumpoto, nʼkukadutsa ku Sikeroni. Anapitirira mpaka kuphiri la Baala kukafika ku Yabineeli, nʼkukathera kunyanja.
11 Malirewo anakafika kumalo otsetsereka otchedwa Ekironi+ kumpoto, nʼkukadutsa ku Sikeroni. Anapitirira mpaka kuphiri la Baala kukafika ku Yabineeli, nʼkukathera kunyanja.