-
Yoswa 15:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako Kalebe anati: “Aliyense amene agonjetse mzinda wa Kiriyati-seferi nʼkuulanda, ndidzamʼpatsa mwana wanga Akisa, kuti akhale mkazi wake.”
-