Yoswa 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anapempha kuti: “Ndidalitseni, poti mwandipatsa malo akumʼmwera* mundipatsenso Guloti-maimu.”* Atatero, Kalebe anamʼpatsa Guloti Wakumtunda ndi Guloti Wakumunsi.
19 Iye anapempha kuti: “Ndidalitseni, poti mwandipatsa malo akumʼmwera* mundipatsenso Guloti-maimu.”* Atatero, Kalebe anamʼpatsa Guloti Wakumtunda ndi Guloti Wakumunsi.