47 Asidodi+ pamodzi ndi midzi yake yozungulira, ikuluikulu ndi ingʼonoingʼono yomwe, Gaza+ pamodzi ndi midzi yake yozungulira, ikuluikulu ndi ingʼonoingʼono yomwe, mpaka kukafika kuchigwa cha Iguputo ndi ku Nyanja Yaikulu pamodzi ndi dera la mʼmbali mwa nyanjayi.+