Yoswa 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho mbadwa za Yosefe,+ omwe ndi Manase ndi Efuraimu, analandira gawo lawo.+