Yoswa 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tselofekadi+ mwana wa Heferi, mwana wa Giliyadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, analibe ana aamuna, koma aakazi okhaokha. Mayina a anawo anali Mala, Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza. Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:3 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, ptsa. 12-13
3 Tselofekadi+ mwana wa Heferi, mwana wa Giliyadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, analibe ana aamuna, koma aakazi okhaokha. Mayina a anawo anali Mala, Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.