Yoswa 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kumʼmwera kwa malirewo linali gawo la Efuraimu, ndipo kumpoto linali gawo la Manase lomwe linakathera kunyanja.+ Kumpoto, gawo la Manase linakakumana ndi la Aseri, ndipo kumʼmawa linakakumana ndi la Isakara.
10 Kumʼmwera kwa malirewo linali gawo la Efuraimu, ndipo kumpoto linali gawo la Manase lomwe linakathera kunyanja.+ Kumpoto, gawo la Manase linakakumana ndi la Aseri, ndipo kumʼmawa linakakumana ndi la Isakara.