Yoswa 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mizinda yotsatirayi ya mʼgawo la Isakara ndi Aseri, pamodzi ndi anthu ake ndi midzi yake yozungulira, inali ya Manase: Beti-seani, Ibuleamu,+ Dori,+ Eni-dori,+ Taanaki,+ Megido komanso madera atatu amapiri.
11 Mizinda yotsatirayi ya mʼgawo la Isakara ndi Aseri, pamodzi ndi anthu ake ndi midzi yake yozungulira, inali ya Manase: Beti-seani, Ibuleamu,+ Dori,+ Eni-dori,+ Taanaki,+ Megido komanso madera atatu amapiri.