Yoswa 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma ana a Manase analephera kulanda mizindayi, moti Akanani anakakamira kukhalabe mʼderali.+