Yoswa 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana a Yosefe anafunsa Yoswa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwatipatsa gawo limodzi lokha+ kuti likhale cholowa chathu, pomwe tilipo anthu ambiri popeza Yehova akutidalitsabe mpaka pano?”+
14 Ana a Yosefe anafunsa Yoswa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwatipatsa gawo limodzi lokha+ kuti likhale cholowa chathu, pomwe tilipo anthu ambiri popeza Yehova akutidalitsabe mpaka pano?”+