Yoswa 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yoswa anawayankha kuti: “Ngati mulipo ambiri pitani kumtunda kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukagwetse mitengo nʼkutenga deralo, poti dera lamapiri la Efuraimu+ lakucheperani.”
15 Yoswa anawayankha kuti: “Ngati mulipo ambiri pitani kumtunda kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukagwetse mitengo nʼkutenga deralo, poti dera lamapiri la Efuraimu+ lakucheperani.”