Yoswa 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ana a Yosefe anati: “Dera lamapiri silitikwanira, ndiponso Akanani akuchigwa, a ku Beti-seani+ ndi midzi yake yozungulira ndiponso akuchigwa cha Yezereeli+ ali ndi magaleta ankhondo+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa.”
16 Kenako ana a Yosefe anati: “Dera lamapiri silitikwanira, ndiponso Akanani akuchigwa, a ku Beti-seani+ ndi midzi yake yozungulira ndiponso akuchigwa cha Yezereeli+ ali ndi magaleta ankhondo+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa.”