Yoswa 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Alevi sadzapatsidwa gawo pakati panu,+ chifukwa cholowa chawo ndi unsembe wa Yehova.+ Fuko la Gadi, Rubeni ndi hafu ya fuko la Manase+ analandira kale cholowa chawo, chimene Mose mtumiki wa Yehova anawapatsa kutsidya lakumʼmawa la Yorodano.” Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:7 Nsanja ya Olonda,9/15/2011, ptsa. 7-8
7 Koma Alevi sadzapatsidwa gawo pakati panu,+ chifukwa cholowa chawo ndi unsembe wa Yehova.+ Fuko la Gadi, Rubeni ndi hafu ya fuko la Manase+ analandira kale cholowa chawo, chimene Mose mtumiki wa Yehova anawapatsa kutsidya lakumʼmawa la Yorodano.”