Yoswa 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho amuna aja anakonzeka kuti azipita, ndipo Yoswa anawalamula kuti: “Pitani mukayendere dzikolo nʼkulemba mmene lilili. Mukatero mukabwere kuno, ndipo ndidzakuchitirani maere pamaso pa Yehova ku Silo kuno.”+
8 Choncho amuna aja anakonzeka kuti azipita, ndipo Yoswa anawalamula kuti: “Pitani mukayendere dzikolo nʼkulemba mmene lilili. Mukatero mukabwere kuno, ndipo ndidzakuchitirani maere pamaso pa Yehova ku Silo kuno.”+