Yoswa 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Yoswa anawachitira maere pamaso pa Yehova ku Silo+ ndipo anagawira Aisiraeli dzikolo moti fuko lililonse analipatsa gawo limodzi.+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:10 Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu,11/2021, tsa. 2
10 Kenako Yoswa anawachitira maere pamaso pa Yehova ku Silo+ ndipo anagawira Aisiraeli dzikolo moti fuko lililonse analipatsa gawo limodzi.+