Yoswa 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kumpoto, malire a gawo lawo anayambira ku Yorodano nʼkupitirira kukafika kumalo otsetsereka akumpoto kwa Yeriko,+ nʼkukwera phiri chakumadzulo, nʼkukathera kuchipululu cha Beti-aveni.+
12 Kumpoto, malire a gawo lawo anayambira ku Yorodano nʼkupitirira kukafika kumalo otsetsereka akumpoto kwa Yeriko,+ nʼkukwera phiri chakumadzulo, nʼkukathera kuchipululu cha Beti-aveni.+