-
Yoswa 19:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 ndiponso midzi yonse yozungulira mizinda imeneyi mpaka kukafika ku Baalati-beere, komwe ndi ku Rama wakumʼmwera. Ichi chinali cholowa cha fuko la Simiyoni motsatira mabanja awo.
-