-
Yoswa 19:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Malirewa analowera chakumadzulo, kukafika ku Marala ndipo anapitirira mpaka ku Dabeseti komanso kuchigwa chimene chili kutsogolo kwa Yokineamu.
-