Yoswa 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuchokera ku Saridi analowera kumʼmawa mpaka kumalire a Kisilotu-tabori. Ndiyeno anapitirira kukafika ku Daberati+ mpaka ku Yafiya.
12 Kuchokera ku Saridi analowera kumʼmawa mpaka kumalire a Kisilotu-tabori. Ndiyeno anapitirira kukafika ku Daberati+ mpaka ku Yafiya.