Yoswa 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Alameleki, Amadi ndi Misali. Analowera kumadzulo nʼkukafika ku Karimeli+ ndi ku Sihori-libanati.