-
Yoswa 19:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 Choncho anamaliza kugawa dzikolo ndipo fuko lililonse linali ndi cholowa chake. Kenako Aisiraeli anamʼpatsa Yoswa mwana wa Nuni cholowa chake pakati pawo.
-