Yoswa 19:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Molamulidwa ndi Yehova, anamʼpatsa mzinda umene anapempha wa Timinati-sera,+ mʼdera lamapiri la Efuraimu ndipo iye anamanga mzindawo nʼkumakhalamo.
50 Molamulidwa ndi Yehova, anamʼpatsa mzinda umene anapempha wa Timinati-sera,+ mʼdera lamapiri la Efuraimu ndipo iye anamanga mzindawo nʼkumakhalamo.