Yoswa 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Azithawira kumzinda umodzi mwa mizindayi.+ Akatero azikaima pageti+ nʼkufotokoza nkhani yake kwa akulu a mzindawo. Akuluwo azimulandira nʼkumupatsa malo mumzindamo ndipo azikhala nawo limodzi.
4 Azithawira kumzinda umodzi mwa mizindayi.+ Akatero azikaima pageti+ nʼkufotokoza nkhani yake kwa akulu a mzindawo. Akuluwo azimulandira nʼkumupatsa malo mumzindamo ndipo azikhala nawo limodzi.