Yoswa 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Atachita maere, maerewo anagwera mabanja a Akohati.+ Ndipo Alevi, omwe anali ana a wansembe Aroni, anapatsidwa mizinda 13 kuchokera mʼmafuko a Yuda,+ Simiyoni+ ndi Benjamini.+
4 Atachita maere, maerewo anagwera mabanja a Akohati.+ Ndipo Alevi, omwe anali ana a wansembe Aroni, anapatsidwa mizinda 13 kuchokera mʼmafuko a Yuda,+ Simiyoni+ ndi Benjamini.+