Yoswa 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anawapatsa Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni.+ (Ariba anali bambo wa Anaki.) Mzindawu pamodzi ndi malo ouzungulira odyetserako ziweto unali mʼdera lamapiri la Yuda.
11 Anawapatsa Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni.+ (Ariba anali bambo wa Anaki.) Mzindawu pamodzi ndi malo ouzungulira odyetserako ziweto unali mʼdera lamapiri la Yuda.