Yoswa 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma malo ena onse amumzindawo komanso midzi yake, anawapereka kwa Kalebe mwana wa Yefune kuti akhale ake.+
12 Koma malo ena onse amumzindawo komanso midzi yake, anawapereka kwa Kalebe mwana wa Yefune kuti akhale ake.+