Yoswa 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a wansembe Aroni anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake,+ wa Heburoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Anawapatsanso Libina+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
13 Ana a wansembe Aroni anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake,+ wa Heburoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Anawapatsanso Libina+ ndi malo ake odyetserako ziweto,