Yoswa 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aini+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Yuta+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Beti-semesi ndi malo ake odyetserako ziweto. Panali mizinda 9 kuchokera mʼmafuko awiri amenewa.
16 Aini+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Yuta+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Beti-semesi ndi malo ake odyetserako ziweto. Panali mizinda 9 kuchokera mʼmafuko awiri amenewa.