Yoswa 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Aijaloni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Gati-rimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.
24 Aijaloni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Gati-rimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.