Yoswa 21:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mizinda yonse ya Alevi mʼdziko limene Aisiraeli anapatsidwa inalipo 48, pamodzi ndi malo ake odyetserako ziweto.+
41 Mizinda yonse ya Alevi mʼdziko limene Aisiraeli anapatsidwa inalipo 48, pamodzi ndi malo ake odyetserako ziweto.+