Yoswa 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Panopa Yehova Mulungu wanu wapatsa abale anu mpumulo mogwirizana ndi zimene anawalonjeza.+ Choncho bwererani, mupite kumatenti anu kudera limene Mose mtumiki wa Yehova anakupatsani, kutsidya lina* la Yorodano.+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:4 Mawu a Mulungu, ptsa. 92-94
4 Panopa Yehova Mulungu wanu wapatsa abale anu mpumulo mogwirizana ndi zimene anawalonjeza.+ Choncho bwererani, mupite kumatenti anu kudera limene Mose mtumiki wa Yehova anakupatsani, kutsidya lina* la Yorodano.+