Yoswa 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Akani+ mwana wa Zera atachita zosakhulupirika potenga zinthu zoyenera kuwonongedwa, kodi mkwiyo sunagwere gulu lonse la Aisiraeli?+ Ndipo iye sanafe yekha chifukwa cha cholakwa chakecho.’”+
20 Akani+ mwana wa Zera atachita zosakhulupirika potenga zinthu zoyenera kuwonongedwa, kodi mkwiyo sunagwere gulu lonse la Aisiraeli?+ Ndipo iye sanafe yekha chifukwa cha cholakwa chakecho.’”+