Yoswa 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atamva zimenezi, anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase anayankha atsogoleri a masauzande a Aisiraeliwo, kuti:+
21 Atamva zimenezi, anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase anayankha atsogoleri a masauzande a Aisiraeliwo, kuti:+