Yoswa 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yehova, Mulungu wa milungu! Yehova, Mulungu wa milungu!+ Iye akudziwa ndipo nawonso Aisiraeli adziwa. Ngati tachita zimenezi chifukwa chopanduka ndiponso chifukwa choti ndife osakhulupirika kwa Yehova, musatisiye amoyo lero.
22 “Yehova, Mulungu wa milungu! Yehova, Mulungu wa milungu!+ Iye akudziwa ndipo nawonso Aisiraeli adziwa. Ngati tachita zimenezi chifukwa chopanduka ndiponso chifukwa choti ndife osakhulupirika kwa Yehova, musatisiye amoyo lero.