-
Yoswa 22:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Koma ife tinamanga guwa lansembeli chifukwa choda nkhawa kuti, ‘Mʼtsogolo muno ana anu adzauza ana athu kuti: “Mulibe ufulu woti muzilambira Yehova Mulungu wa Isiraeli.
-